Numeri 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Itanitsa fuko la Levi+ ndipo uwapereke kwa wansembe Aroni kuti azimutumikira.+ Numeri 4:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 kuyambira azaka 30 mpaka 50,+ onse ogwira ntchito yolemetsa ndi utumiki wonyamula katundu m’chihema chokumanako,+
47 kuyambira azaka 30 mpaka 50,+ onse ogwira ntchito yolemetsa ndi utumiki wonyamula katundu m’chihema chokumanako,+