Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 4:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Aroni ndi ana ake akamaliza kuphimba zinthu za m’malo oyera+ ndi ziwiya zonse+ za m’malo oyerawo posamutsa msasa, ana a Kohati azilowamo n’kudzazinyamula.+ Iwo asamakhudze+ zinthu za m’malo oyerazo chifukwa angafe. Zinthu zimenezi ndizo katundu wa m’chihema chokumanako amene ana a Kohati azinyamula.+

  • Numeri 4:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Tsopano utumiki umene mabanja a Agerisoni azichita ndiponso katundu amene azinyamula ndi uwu:+

  • Numeri 4:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Tsopano uyu ndi katundu amene azinyamula,+ monga gawo la utumiki wawo m’chihema chokumanako: Mafelemu+ a chihema chopatulika, mipiringidzo yake,+ mizati yake,+ ndiponso zitsulo zokhazikapo mizati ndi mafelemu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena