Ekisodo 26:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Upangenso mipiringidzo ya mtengo wa mthethe,+ mipiringidzo isanu yogwira mafelemu a mbali imodzi ya chihema chopatulika. Ekisodo 36:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiyeno anapanga mipiringidzo yamtengo wa mthethe, mipiringidzo isanu yogwira mafelemu a mbali imodzi ya chihema chopatulika,+
26 “Upangenso mipiringidzo ya mtengo wa mthethe,+ mipiringidzo isanu yogwira mafelemu a mbali imodzi ya chihema chopatulika.
31 Ndiyeno anapanga mipiringidzo yamtengo wa mthethe, mipiringidzo isanu yogwira mafelemu a mbali imodzi ya chihema chopatulika,+