Numeri 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamene msasa ukusamuka, Aroni ndi ana ake azilowa m’chihema. Mmenemo, azichotsa nsalu yotchinga+ n’kuphimba nayo likasa+ la umboni.
5 Pamene msasa ukusamuka, Aroni ndi ana ake azilowa m’chihema. Mmenemo, azichotsa nsalu yotchinga+ n’kuphimba nayo likasa+ la umboni.