Numeri 4:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Anawerenga kuyambira azaka 30 mpaka 50, ndipo onse anasankhidwa kuti azitumikira komanso kunyamula katundu wa pachihema chokumanako.+
47 Anawerenga kuyambira azaka 30 mpaka 50, ndipo onse anasankhidwa kuti azitumikira komanso kunyamula katundu wa pachihema chokumanako.+