Numeri 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Muwerenge kuyambira azaka 30+ mpaka 50,+ onse olowa m’gulu la ogwira ntchito+ m’chihema chokumanako. Numeri 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Uwerenge kuyambira azaka 30 mpaka 50,+ onse olowa m’gulu la ogwira ntchito m’chihema chokumanako. Numeri 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Uwerenge kuyambira azaka 30 mpaka 50, onse olowa m’gulu la ogwira ntchito pachihema chokumanako.+
3 Muwerenge kuyambira azaka 30+ mpaka 50,+ onse olowa m’gulu la ogwira ntchito+ m’chihema chokumanako.