1 Mbiri 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atatero, Alevi anawerengedwa kuyambira azaka 30 kupita m’tsogolo.+ Anawerenga mwamuna aliyense wamphamvu, mmodzi ndi mmodzi,* ndipo onse anakwana 38,000. Luka 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamene Yesu anayamba ntchito yake,+ anali ndi zaka pafupifupi 30.+ Anthu ankakhulupirira kuti Yesu analimwana+ wa Yosefe,+mwana wa Heli,
3 Atatero, Alevi anawerengedwa kuyambira azaka 30 kupita m’tsogolo.+ Anawerenga mwamuna aliyense wamphamvu, mmodzi ndi mmodzi,* ndipo onse anakwana 38,000.
23 Pamene Yesu anayamba ntchito yake,+ anali ndi zaka pafupifupi 30.+ Anthu ankakhulupirira kuti Yesu analimwana+ wa Yosefe,+mwana wa Heli,