Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Yakobo anabereka Yosefe mwamuna wake wa Mariya, amene anabereka Yesu,+ wotchedwa Khristu.+

  • Luka 1:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Poyankha mngeloyo anauza Mariya kuti: “Mzimu woyera+ udzafika pa iwe, ndipo mphamvu ya Wam’mwambamwamba idzakuphimba. Pa chifukwa chimenechinso, wodzabadwayo adzatchedwa woyera,+ Mwana wa Mulungu.+

  • Luka 4:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pamenepo onse anayamba kumutamanda ndi kudabwa ndi mawu ogwira mtima+ otuluka pakamwa pake, mwakuti anali kunena kuti: “Kodi iyeyu si mwana wa Yosefe?”+

  • Yohane 6:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Iwo anayamba kunena kuti:+ “Kodi uyu si Yesu mwana wa Yosefe,+ amene bambo ake ndi mayi ake tikuwadziwa? Nanga bwanji pano akunena kuti, ‘Ndinatsika kumwamba’?”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena