Mateyu 14:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Pamenepo amene anali m’ngalawamo anam’gwadira ndi kunena kuti: “Ndinudi Mwana wa Mulungu.”+ Yohane 1:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndipo ine ndaonadi zimenezo, ndachitira umboni ndithu kuti iyeyu ndi Mwana wa Mulungu.”+ Yohane 20:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma izi zalembedwa+ kuti mukhulupirire kuti Yesu alidi Khristu Mwana wa Mulungu, ndi kutinso, mwa kukhulupirira,+ mukhale ndi moyo m’dzina lake. Aroma 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 koma amene Mulungu mwa mphamvu+ yake anam’lengeza kukhala Mwana wake+ mwa mzimu woyera+ pomuukitsa kwa akufa.+ Ameneyu ndi Yesu Khristu Ambuye wathu.
31 Koma izi zalembedwa+ kuti mukhulupirire kuti Yesu alidi Khristu Mwana wa Mulungu, ndi kutinso, mwa kukhulupirira,+ mukhale ndi moyo m’dzina lake.
4 koma amene Mulungu mwa mphamvu+ yake anam’lengeza kukhala Mwana wake+ mwa mzimu woyera+ pomuukitsa kwa akufa.+ Ameneyu ndi Yesu Khristu Ambuye wathu.