Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 13:54
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 54 Atafika m’dera lakwawo+ anayamba kuwaphunzitsa m’sunagoge wawo,+ moti anthu anadabwa ndipo anali kunena kuti: “Kodi munthu ameneyu, nzeru ndi ntchito zamphamvu zoterezi anazitenga kuti?

  • Maliko 6:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Sabata itafika, iye anayamba kuphunzitsa m’sunagoge. Anthu ambiri amene anali kumvetsera, anadabwa ndipo anali kunena kuti: “Kodi munthu ameneyu anazitenga kuti zinthu zimenezi?+ Ndipo n’chifukwa chiyani nzeru zimenezi zinaperekedwa kwa munthu ameneyu, ndi kuti azitha kuchita ntchito zamphamvu zoterezi?

  • Yohane 6:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Iwo anayamba kunena kuti:+ “Kodi uyu si Yesu mwana wa Yosefe,+ amene bambo ake ndi mayi ake tikuwadziwa? Nanga bwanji pano akunena kuti, ‘Ndinatsika kumwamba’?”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena