2 Sabata litakwana, iye anayamba kuphunzitsa musunagoge. Anthu ambiri amene anamumvetsera anadabwa ndipo ananena kuti: “Kodi munthu ameneyu anazitenga kuti zinthu zimenezi?+ Ndipo nʼchifukwa chiyani nzeru zimenezi zinaperekedwa kwa iyeyu, komanso kuti azitha kuchita ntchito zamphamvu zoterezi?+