Yohane 6:69 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 69 Ife takhulupirira ndipo tadziwa kuti inu ndinu Woyera wa Mulungu.”+ Yohane 10:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 nanga kodi inu mukundiuza ine woyeretsedwa ndi Atate ndi kutumizidwa m’dziko kuti, ‘Ukunyoza Mulungu,’ chifukwa ndanena kuti, Ndine Mwana wa Mulungu?+
36 nanga kodi inu mukundiuza ine woyeretsedwa ndi Atate ndi kutumizidwa m’dziko kuti, ‘Ukunyoza Mulungu,’ chifukwa ndanena kuti, Ndine Mwana wa Mulungu?+