Numeri 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Muwerenge onse kuyambira azaka 30+ mpaka 50,+ amene ali mʼgulu la anthu amene anasankhidwa kuti azigwira ntchito mʼchihema chokumanako.+
3 Muwerenge onse kuyambira azaka 30+ mpaka 50,+ amene ali mʼgulu la anthu amene anasankhidwa kuti azigwira ntchito mʼchihema chokumanako.+