-
Numeri 4:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Muwerenge onse kuyambira azaka 30 mpaka 50, amene ali mʼgulu la anthu amene anasankhidwa kuti azigwira ntchito mʼchihema chokumanako.
-