Numeri 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Uwerenge kuyambira azaka 30 mpaka 50,+ onse olowa m’gulu la ogwira ntchito m’chihema chokumanako.