Numeri 16:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Chotero, wansembe Eleazara anatenga zofukizira+ zamkuwa zimene anabwera nazo anthu amene anapsa ndi moto aja, ndipo anazisula n’kuzipanga timalata tokutira guwa lansembe.
39 Chotero, wansembe Eleazara anatenga zofukizira+ zamkuwa zimene anabwera nazo anthu amene anapsa ndi moto aja, ndipo anazisula n’kuzipanga timalata tokutira guwa lansembe.