Numeri 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mudzachite izi: Iwe Kora ndi khamu lonselo,+ mudzatenge zofukizira.+