38 Uyu ndi amene+ anali pakati pa mpingo+ m’chipululu limodzi ndi mngelo+ amene analankhula ndi iyeyu komanso makolo athu paphiri la Sinai. Pamenepo analandira mawu opatulika+ omwe ndi amphamvu kuti awapereke kwa inu.
2 Iye anali wokhulupirika+ kwa Mulungu amene anamuika kukhala mtumwi ndi mkulu wa ansembe, monga mmenenso Mose+ analili wokhulupirika m’nyumba yonse ya Mulungu.+