11 Ngati wina akulankhula, alankhule monga mwa mawu opatulika+ a Mulungu. Ngati wina akutumikira,+ atumikire modalira mphamvu imene Mulungu amapereka,+ kuti m’zinthu zonse Mulungu alemekezeke+ kudzera mwa Yesu Khristu. Ulemerero+ ndi mphamvu, ndi zake mpaka muyaya. Ame.