Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 19:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Pamene kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosako kunali kupitiriza kukwererakwerera, Mose anayamba kulankhula, ndipo Mulungu woona anamuyankha ndi mawu amphamvu.+

  • Deuteronomo 4:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 za tsiku limene munaimirira pamaso pa Yehova Mulungu wanu ku Horebe,+ pamene Yehova anandiuza kuti, ‘Sonkhanitsa anthu kwa ine kuti amve mawu anga,+ naphunzire kundiopa+ masiku onse amene iwo adzakhala ndi moyo padziko, ndi kuti aphunzitsenso ana awo.’+

  • Deuteronomo 4:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pamenepo Yehova anayamba kukulankhulani kuchokera pakati pa moto.+ Inu munamva mawu koma simunaone kalikonse.+ Munangomva mawu osaona kalikonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena