Ekisodo 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Tamvera! Nditsikira kwa iwe mumtambo wakuda,+ kuti anthu amve pamene ndikulankhula ndi iwe,+ ndi kuti iwenso azikukhulupirira nthawi zonse.”+ Choncho Mose anali atanena mawu a anthuwo kwa Yehova. Aheberi 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Samalani kuti musasiye kumvetsera wolankhulayo.+ Pakuti ngati amene analephera kumvera wopereka chenjezo la Mulungu padziko lapansi sanapulumuke,+ kuli bwanji ifeyo? Nafenso sitidzapulumuka tikachoka kwa iye amene amalankhula ali kumwamba.+
9 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Tamvera! Nditsikira kwa iwe mumtambo wakuda,+ kuti anthu amve pamene ndikulankhula ndi iwe,+ ndi kuti iwenso azikukhulupirira nthawi zonse.”+ Choncho Mose anali atanena mawu a anthuwo kwa Yehova.
25 Samalani kuti musasiye kumvetsera wolankhulayo.+ Pakuti ngati amene analephera kumvera wopereka chenjezo la Mulungu padziko lapansi sanapulumuke,+ kuli bwanji ifeyo? Nafenso sitidzapulumuka tikachoka kwa iye amene amalankhula ali kumwamba.+