-
Ekisodo 19:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Tamvera! Ndibwera kwa iwe mumtambo wakuda kuti anthu azimva ndikamalankhula nawe komanso kuti azikukhulupirira nthawi zonse.” Apa nʼkuti Mose atanena mawu a anthuwo kwa Yehova.
-