Ekisodo 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Tamvera! Nditsikira kwa iwe mumtambo wakuda,+ kuti anthu amve pamene ndikulankhula ndi iwe,+ ndi kuti iwenso azikukhulupirira nthawi zonse.”+ Choncho Mose anali atanena mawu a anthuwo kwa Yehova.
9 Pamenepo Yehova anauza Mose kuti: “Tamvera! Nditsikira kwa iwe mumtambo wakuda,+ kuti anthu amve pamene ndikulankhula ndi iwe,+ ndi kuti iwenso azikukhulupirira nthawi zonse.”+ Choncho Mose anali atanena mawu a anthuwo kwa Yehova.