Deuteronomo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Chotero musamale moyo wanu,+ chifukwa pa tsiku limene Yehova analankhula nanu kuchokera pakati pa moto ku Horebe, simunaone kalikonse+ m’motomo. Yesaya 40:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi anthu inu Mulungu mungamuyerekezere ndi ndani,+ ndipo kodi mungapange chiyani choti mumufanizire nacho?+ Yohane 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Palibe munthu anaonapo Mulungu ndi kale lonse,+ mulungu wobadwa yekha+ amene ali pachifuwa+ cha Atate ndiye amene anafotokoza za Mulungu.+ Yohane 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mulungu ndiye Mzimu,+ ndipo onse omulambira ayenera kumulambira motsogoleredwa ndi mzimu ndi choonadi.”+
15 “Chotero musamale moyo wanu,+ chifukwa pa tsiku limene Yehova analankhula nanu kuchokera pakati pa moto ku Horebe, simunaone kalikonse+ m’motomo.
18 Kodi anthu inu Mulungu mungamuyerekezere ndi ndani,+ ndipo kodi mungapange chiyani choti mumufanizire nacho?+
18 Palibe munthu anaonapo Mulungu ndi kale lonse,+ mulungu wobadwa yekha+ amene ali pachifuwa+ cha Atate ndiye amene anafotokoza za Mulungu.+
24 Mulungu ndiye Mzimu,+ ndipo onse omulambira ayenera kumulambira motsogoleredwa ndi mzimu ndi choonadi.”+