Ekisodo 20:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti:+ “Ana a Isiraeli uwauze kuti, ‘Mwadzionera nokha kuti ine ndalankhula nanu kuchokera kumwamba.+ Aheberi 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Simunafike paphiri limene panamveka kulira kwa lipenga+ ndi mawu a winawake akulankhula,+ amene anthu atawamva, anachonderera kuti asawauzenso mawu ena.+
22 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti:+ “Ana a Isiraeli uwauze kuti, ‘Mwadzionera nokha kuti ine ndalankhula nanu kuchokera kumwamba.+
19 Simunafike paphiri limene panamveka kulira kwa lipenga+ ndi mawu a winawake akulankhula,+ amene anthu atawamva, anachonderera kuti asawauzenso mawu ena.+