Yoswa 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Patapita nthawi, ndinatumiza Mose ndi Aroni,+ ndipo ndinagwetsera Iguputo miliri.+ Nditatero ndinakutulutsani+ ku Iguputoko. 1 Samueli 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Samueli anauza anthuwo kuti: “Yehova ndiye mboni, iye amene anagwiritsa ntchito Mose ndi Aroni, amenenso anatulutsa makolo anu m’dziko la Iguputo.+
5 Patapita nthawi, ndinatumiza Mose ndi Aroni,+ ndipo ndinagwetsera Iguputo miliri.+ Nditatero ndinakutulutsani+ ku Iguputoko.
6 Ndiyeno Samueli anauza anthuwo kuti: “Yehova ndiye mboni, iye amene anagwiritsa ntchito Mose ndi Aroni, amenenso anatulutsa makolo anu m’dziko la Iguputo.+