Ekisodo 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Umenewu ndiwo mzere wa Aroni ndi Mose, amene Yehova anawauza kuti:+ “Tulutsani ana a Isiraeli m’dziko la Iguputo malinga ndi makamu awo.”+ Nehemiya 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munawaphunzitsa za sabata lanu lopatulika.+ Munawapatsa malangizo, mfundo ndi chilamulo kudzera mwa Mose mtumiki wanu.+ Salimo 77:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwatsogolera anthu anu ngati nkhosa,+Kudzera mwa Mose ndi Aroni.+ Salimo 105:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno anatumiza Mose mtumiki wake,+Ndi Aroni amene anamusankha.+ Hoseya 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova anatulutsa Isiraeli ku Iguputo pogwiritsa ntchito mneneri,+ ndipo mneneri analondera Isiraeli.+ Mika 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo,+ ndipo ndinakuwombolani m’nyumba ya akapolo.+ Ndinakutumizirani Mose, Aroni ndi Miriamu kuti akutsogolereni.+
26 Umenewu ndiwo mzere wa Aroni ndi Mose, amene Yehova anawauza kuti:+ “Tulutsani ana a Isiraeli m’dziko la Iguputo malinga ndi makamu awo.”+
14 Munawaphunzitsa za sabata lanu lopatulika.+ Munawapatsa malangizo, mfundo ndi chilamulo kudzera mwa Mose mtumiki wanu.+
13 Yehova anatulutsa Isiraeli ku Iguputo pogwiritsa ntchito mneneri,+ ndipo mneneri analondera Isiraeli.+
4 Ine ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo,+ ndipo ndinakuwombolani m’nyumba ya akapolo.+ Ndinakutumizirani Mose, Aroni ndi Miriamu kuti akutsogolereni.+