Ekisodo 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova anali kuyenda patsogolo pawo mumtambo woima njo ngati chipilala powatsogolera usana,+ ndipo usiku anali kuwatsogolera m’moto woima njo ngati chipilala kuti uziwaunikira, kuti apitirizebe ulendo usana ndi usiku.+ Salimo 78:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Kenako anachititsa anthu ake kuchoka m’dzikolo ngati gulu la nkhosa,+Anawayendetsa m’chipululu ngati gulu la ziweto.+ Hoseya 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova anatulutsa Isiraeli ku Iguputo pogwiritsa ntchito mneneri,+ ndipo mneneri analondera Isiraeli.+
21 Yehova anali kuyenda patsogolo pawo mumtambo woima njo ngati chipilala powatsogolera usana,+ ndipo usiku anali kuwatsogolera m’moto woima njo ngati chipilala kuti uziwaunikira, kuti apitirizebe ulendo usana ndi usiku.+
52 Kenako anachititsa anthu ake kuchoka m’dzikolo ngati gulu la nkhosa,+Anawayendetsa m’chipululu ngati gulu la ziweto.+
13 Yehova anatulutsa Isiraeli ku Iguputo pogwiritsa ntchito mneneri,+ ndipo mneneri analondera Isiraeli.+