Salimo 77:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwatsogolera anthu anu ngati nkhosa,+Kudzera mwa Mose ndi Aroni.+ Salimo 105:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ndiyeno anayamba kuwatulutsa atatenga siliva ndi golide.+Pakati pa mafuko ake panalibe amene anapunthwa panjira. Salimo 136:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yamikani amene anatulutsa Aisiraeli pakati pawo:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
37 Ndiyeno anayamba kuwatulutsa atatenga siliva ndi golide.+Pakati pa mafuko ake panalibe amene anapunthwa panjira.
11 Yamikani amene anatulutsa Aisiraeli pakati pawo:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+