Ekisodo 12:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Ndipo pa tsiku limeneli, Yehova anatulutsa ana a Isiraeli malinga ndi makamu awo+ m’dziko la Iguputo. 1 Samueli 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Samueli anauza anthuwo kuti: “Yehova ndiye mboni, iye amene anagwiritsa ntchito Mose ndi Aroni, amenenso anatulutsa makolo anu m’dziko la Iguputo.+ Salimo 78:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Kenako anachititsa anthu ake kuchoka m’dzikolo ngati gulu la nkhosa,+Anawayendetsa m’chipululu ngati gulu la ziweto.+
51 Ndipo pa tsiku limeneli, Yehova anatulutsa ana a Isiraeli malinga ndi makamu awo+ m’dziko la Iguputo.
6 Ndiyeno Samueli anauza anthuwo kuti: “Yehova ndiye mboni, iye amene anagwiritsa ntchito Mose ndi Aroni, amenenso anatulutsa makolo anu m’dziko la Iguputo.+
52 Kenako anachititsa anthu ake kuchoka m’dzikolo ngati gulu la nkhosa,+Anawayendetsa m’chipululu ngati gulu la ziweto.+