Salimo 136:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yamikani amene anayendetsa anthu ake m’chipululu:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
16 Yamikani amene anayendetsa anthu ake m’chipululu:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+