Ekisodo 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Umenewu ndiwo mzere wa Aroni ndi Mose, amene Yehova anawauza kuti:+ “Tulutsani ana a Isiraeli m’dziko la Iguputo malinga ndi makamu awo.”+ Ekisodo 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chotero Mulungu anachititsa ana a Isiraeli kuyenda njira yaitali yodutsa m’chipululu chapafupi ndi Nyanja Yofiira.+ Koma iwo potuluka m’dziko la Iguputo, anayenda mwa dongosolo lomenyera nkhondo.+
26 Umenewu ndiwo mzere wa Aroni ndi Mose, amene Yehova anawauza kuti:+ “Tulutsani ana a Isiraeli m’dziko la Iguputo malinga ndi makamu awo.”+
18 Chotero Mulungu anachititsa ana a Isiraeli kuyenda njira yaitali yodutsa m’chipululu chapafupi ndi Nyanja Yofiira.+ Koma iwo potuluka m’dziko la Iguputo, anayenda mwa dongosolo lomenyera nkhondo.+