Ekisodo 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lankhula ndi ana a Isiraeli kuti abwerere ndi kumanga msasa pafupi ndi Pihahiroti, pakati pa Migidoli ndi nyanja, koma moyang’anizana ndi Baala-zefoni.+ Mumange msasa wanu pafupi ndi nyanja, patsogolo pa Baala-zefoni. Numeri 33:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero ana a Isiraeli ananyamuka ku Ramese+ n’kukamanga msasa ku Sukoti.+
2 “Lankhula ndi ana a Isiraeli kuti abwerere ndi kumanga msasa pafupi ndi Pihahiroti, pakati pa Migidoli ndi nyanja, koma moyang’anizana ndi Baala-zefoni.+ Mumange msasa wanu pafupi ndi nyanja, patsogolo pa Baala-zefoni.