Ekisodo 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Miriamu, mneneri wamkazi, mlongo wake wa Aroni,+ anatenga maseche m’manja mwake,+ ndipo akazi ena onse anam’tsatira akuimba maseche ndi kuvina.+ Numeri 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano Miriamu ndi Aroni anayamba kum’nena Mose chifukwa cha mkazi wachikusi amene anam’kwatira.+
20 Kenako Miriamu, mneneri wamkazi, mlongo wake wa Aroni,+ anatenga maseche m’manja mwake,+ ndipo akazi ena onse anam’tsatira akuimba maseche ndi kuvina.+
12 Tsopano Miriamu ndi Aroni anayamba kum’nena Mose chifukwa cha mkazi wachikusi amene anam’kwatira.+