Ekisodo 12:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Ndipo pa tsiku limeneli, Yehova anatulutsa ana a Isiraeli malinga ndi makamu awo+ m’dziko la Iguputo. Deuteronomo 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Musachite zimenezo chifukwa Yehova ndiye anakutengani n’kukutulutsani m’ng’anjo yachitsulo,+ mu Iguputo, kuti mukhale anthu akeake+ monga mmene zilili lero. Machitidwe 7:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Munthu ameneyo anawatsogolera ndi kutuluka nawo,+ atachita zodabwitsa ndi zizindikiro mu Iguputo,+ pa Nyanja Yofiira+ ndi m’chipululu kwa zaka 40.+
51 Ndipo pa tsiku limeneli, Yehova anatulutsa ana a Isiraeli malinga ndi makamu awo+ m’dziko la Iguputo.
20 Musachite zimenezo chifukwa Yehova ndiye anakutengani n’kukutulutsani m’ng’anjo yachitsulo,+ mu Iguputo, kuti mukhale anthu akeake+ monga mmene zilili lero.
36 Munthu ameneyo anawatsogolera ndi kutuluka nawo,+ atachita zodabwitsa ndi zizindikiro mu Iguputo,+ pa Nyanja Yofiira+ ndi m’chipululu kwa zaka 40.+