Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 19:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+

  • Deuteronomo 9:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Pamenepo ndinayamba kupembedzera+ Yehova ndi kunena kuti, ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, musawononge anthu anu, amene ndiwo chuma chanu chapadera,+ anthu amene munawawombola ndi mphamvu yanu, amene munawatulutsa mu Iguputo+ ndi dzanja lamphamvu.+

  • 1 Mafumu 8:53
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 53 Pakuti inuyo munawapatula pakati pa mitundu yonse ya anthu a padziko lapansi+ kuti akhale cholowa chanu, monga momwe munalankhulira kudzera mwa Mose+ mtumiki wanu, pamene munali kutulutsa makolo athu ku Iguputo, inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.”

  • Salimo 135:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ya wadzisankhira Yakobo,+

      Wadzisankhira Isiraeli kukhala chuma chake chapadera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena