Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 5:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Yehova analankhula nanu pamasom’pamaso m’phiri, kuchokera pakati pa moto.+

  • Yesaya 63:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pamene iwo anali kuvutika m’masautso awo onse, iyenso anali kuvutika.+ Mthenga amene iye anawatumizira, anawapulumutsa.+ Chifukwa cha chikondi chake ndi chisoni chake, iye anawawombola.+ Anawakweza m’mwamba ndi kuwanyamula masiku onse akale.+

  • Machitidwe 7:53
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 53 inu amene munalandira Chilamulo kudzera mwa angelo,+ koma osachisunga.”

  • Agalatiya 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Nanga tsopano Chilamulo chinakhalapo chifukwa chiyani? Anachiwonjezerapo kuti machimo aonekere,+ mpaka amene ali mbewuyo atafika,+ amene anapatsidwa lonjezolo. Ndipo Chilamulocho chinaperekedwa kudzera mwa angelo,+ kudzeranso m’dzanja la mkhalapakati.+

  • Aheberi 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pakuti ngati mawu amene angelo ananena+ analidi osagwedezeka, ndipo pa tchimo lililonse ndi kusamvera kulikonse, chilango chinaperekedwa mogwirizana ndi chilungamo,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena