Aheberi 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chifukwa ngati mawu amene angelo ananena+ analidi oona, ndipo chilango chinaperekedwa mwachilungamo pa tchimo lililonse ndi kusamvera kulikonse,+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:2 Nsanja ya Olonda,5/1/1990, tsa. 30
2 Chifukwa ngati mawu amene angelo ananena+ analidi oona, ndipo chilango chinaperekedwa mwachilungamo pa tchimo lililonse ndi kusamvera kulikonse,+