Aheberi 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti ngati mawu amene angelo ananena+ analidi osagwedezeka, ndipo pa tchimo lililonse ndi kusamvera kulikonse, chilango chinaperekedwa mogwirizana ndi chilungamo,+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:2 Nsanja ya Olonda,5/1/1990, tsa. 30
2 Pakuti ngati mawu amene angelo ananena+ analidi osagwedezeka, ndipo pa tchimo lililonse ndi kusamvera kulikonse, chilango chinaperekedwa mogwirizana ndi chilungamo,+