Deuteronomo 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Inu munaona ndi maso anu zimene Yehova anachita pa nkhani ya Baala wa ku Peori, kuti munthu aliyense amene anatsatira Baala wa ku Peori,+ Yehova Mulungu wanu anamuwononga ndi kum’chotsa pakati panu.+ 1 Akorinto 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano zinthu zimenezi zinali kuwagwera monga zitsanzo, ndipo zinalembedwa kuti zitichenjeze+ ifeyo amene mapeto a nthawi* zino atifikira.+ Yuda 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ngakhale kuti mukudziwa kale zinthu zonse, ndikufuna kukukumbutsani kuti,+ ngakhale kuti Yehova anapulumutsa anthu ake powatulutsa m’dziko la Iguputo,+ pambuyo pake anawononga amene analibe chikhulupiriro.+
3 “Inu munaona ndi maso anu zimene Yehova anachita pa nkhani ya Baala wa ku Peori, kuti munthu aliyense amene anatsatira Baala wa ku Peori,+ Yehova Mulungu wanu anamuwononga ndi kum’chotsa pakati panu.+
11 Tsopano zinthu zimenezi zinali kuwagwera monga zitsanzo, ndipo zinalembedwa kuti zitichenjeze+ ifeyo amene mapeto a nthawi* zino atifikira.+
5 Ngakhale kuti mukudziwa kale zinthu zonse, ndikufuna kukukumbutsani kuti,+ ngakhale kuti Yehova anapulumutsa anthu ake powatulutsa m’dziko la Iguputo,+ pambuyo pake anawononga amene analibe chikhulupiriro.+