Numeri 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero Mose anauza oweruza a mu Isiraeli+ kuti: “Aliyense wa inu aphe+ anthu ake amene akukapembedza nawo Baala wa ku Peori.” Numeri 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amene anaphedwa ndi mliriwo analipo 24,000.+ 1 Akorinto 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tisamachite dama,+ mmene ena mwa iwo anachitira dama, n’kufa 23,000 tsiku limodzi.+
5 Chotero Mose anauza oweruza a mu Isiraeli+ kuti: “Aliyense wa inu aphe+ anthu ake amene akukapembedza nawo Baala wa ku Peori.”