Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 22:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Wopereka nsembe kwa milungu ina osati kwa Yehova yekha aziphedwa ndithu.+

  • Ekisodo 32:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Pamenepo iye anawauza kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Aliyense wa inu amange lupanga lake m’chiuno mwake. Ndiyeno mudutse mkati mwa msasa ndi kuyenda mobwerezabwereza, kuchoka pachipata china kufika pachipata china, ndipo aliyense wa inu aphe m’bale wake, mnzake ndi mnzake wapamtima.’”+

  • Deuteronomo 13:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 usavomereze zofuna zake kapena kumumvera.+ Diso lako lisamumvere chifundo ndipo usamumvere chisoni+ kapena kum’bisa kuti um’teteze.

  • Deuteronomo 13:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma umuphe ndithu.+ Dzanja lako lizikhala loyamba kum’ponya miyala kuti afe, ndipo anthu ena onse azibwera pambuyo.+

  • 1 Mafumu 18:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Ndiyeno Eliya anauza anthuwo kuti: “Gwirani aneneri a Baala! Muonetsetse kuti pasapezeke wothawa!” Nthawi yomweyo anawagwira, ndipo Eliya anatsetserekera nawo kuchigwa cha Kisoni,+ n’kukawapha kumeneko.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena