Deuteronomo 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma muzimupha ndithu.+ Dzanja lanu lizikhala loyamba kumʼponya miyala kuti afe, ndipo anthu ena onse azibwera pambuyo.+
9 Koma muzimupha ndithu.+ Dzanja lanu lizikhala loyamba kumʼponya miyala kuti afe, ndipo anthu ena onse azibwera pambuyo.+