Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 22:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Wopereka nsembe kwa milungu ina osati kwa Yehova yekha aziphedwa ndithu.+

  • Ekisodo 32:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Pamenepo iye anawauza kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Aliyense wa inu amange lupanga lake m’chiuno mwake. Ndiyeno mudutse mkati mwa msasa ndi kuyenda mobwerezabwereza, kuchoka pachipata china kufika pachipata china, ndipo aliyense wa inu aphe m’bale wake, mnzake ndi mnzake wapamtima.’”+

  • Numeri 25:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Chotero Mose anauza oweruza a mu Isiraeli+ kuti: “Aliyense wa inu aphe+ anthu ake amene akukapembedza nawo Baala wa ku Peori.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena