Numeri 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero Mose anauza oweruza a mu Isiraeli+ kuti: “Aliyense wa inu aphe+ anthu ake amene akukapembedza nawo Baala wa ku Peori.” Deuteronomo 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 usavomereze zofuna zake kapena kumumvera.+ Diso lako lisamumvere chifundo ndipo usamumvere chisoni+ kapena kum’bisa kuti um’teteze. Zekariya 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakadzapezeka munthu aliyense wolosera, bambo ake ndi mayi ake amene anamubereka, adzamuuze kuti, ‘Iwe ufa ndithu, chifukwa walankhula zonama m’dzina la Yehova.’ Ndiyeno bambo ndi mayi akewo adzamulase chifukwa chakuti anali kulosera.+
5 Chotero Mose anauza oweruza a mu Isiraeli+ kuti: “Aliyense wa inu aphe+ anthu ake amene akukapembedza nawo Baala wa ku Peori.”
8 usavomereze zofuna zake kapena kumumvera.+ Diso lako lisamumvere chifundo ndipo usamumvere chisoni+ kapena kum’bisa kuti um’teteze.
3 Pakadzapezeka munthu aliyense wolosera, bambo ake ndi mayi ake amene anamubereka, adzamuuze kuti, ‘Iwe ufa ndithu, chifukwa walankhula zonama m’dzina la Yehova.’ Ndiyeno bambo ndi mayi akewo adzamulase chifukwa chakuti anali kulosera.+