Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 13:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “M’bale wako, amene ndi mwana wamwamuna wa mayi ako, kapena mwana wako wamwamuna, mwana wako wamkazi, mkazi wako wokondedwa kapena bwenzi lako lapamtima,+ akayesa kukupatutsa mwamseri pokuuza kuti, ‘Tiye tikatumikire milungu ina,’+ milungu imene iwe kapena makolo ako sanaidziwe,

  • Deuteronomo 13:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma umuphe ndithu.+ Dzanja lako lizikhala loyamba kum’ponya miyala kuti afe, ndipo anthu ena onse azibwera pambuyo.+

  • Deuteronomo 18:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “‘Koma mneneri amene adzadzikuza mwa kulankhula m’dzina langa mawu amene sindinamulamule kuti alankhule,+ kapena kulankhula m’dzina la milungu ina,+ mneneri ameneyo afe ndithu.+

  • Mateyu 10:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Amene amakonda kwambiri bambo ake kapena mayi ake kuposa ine sali woyenera ine. Komanso amene amakonda kwambiri mwana wake wamwamuna kapena wamkazi kuposa ine sali woyenera ine.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena