Deuteronomo 33:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munthu amene anauza bambo ndi mayi ake kuti, ‘Sindinawaone.’Ngakhale abale ake sanawavomereze,+Ndipo ana ake sanawadziwe.Pakuti anasunga mawu anu,+Ndipo anapitiriza kusunga pangano lanu.+ Mateyu 19:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Aliyense amene wasiya nyumba, abale, alongo, abambo, amayi, ana kapena minda chifukwa cha dzina langa adzalandira zochuluka kwambiri kuposa zimenezi, ndipo adzapeza moyo wosatha.+ Luka 14:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Ngati wina wabwera kwa ine, koma osadana ndi bambo ake, mayi ake, mkazi wake, ana ake, abale ake ndi alongo ake, ngakhale moyo wake umene,+ sangakhale wophunzira wanga.+
9 Munthu amene anauza bambo ndi mayi ake kuti, ‘Sindinawaone.’Ngakhale abale ake sanawavomereze,+Ndipo ana ake sanawadziwe.Pakuti anasunga mawu anu,+Ndipo anapitiriza kusunga pangano lanu.+
29 Aliyense amene wasiya nyumba, abale, alongo, abambo, amayi, ana kapena minda chifukwa cha dzina langa adzalandira zochuluka kwambiri kuposa zimenezi, ndipo adzapeza moyo wosatha.+
26 “Ngati wina wabwera kwa ine, koma osadana ndi bambo ake, mayi ake, mkazi wake, ana ake, abale ake ndi alongo ake, ngakhale moyo wake umene,+ sangakhale wophunzira wanga.+