Maliko 10:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 amene panopa sadzapeza zochuluka kuwirikiza maulendo 100+ m’nthawi* ino. Iye adzapeza nyumba, abale, alongo, amayi, ana ndi minda, limodzi ndi mazunzo,+ ndipo m’nthawi imene ikubwerayo, adzapeza moyo wosatha. Luka 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yesu anawauza kuti: “Ndithu ndikukuuzani, Palibe amene wasiya nyumba, mkazi, abale, makolo kapena ana, chifukwa cha ufumu wa Mulungu+ Luka 18:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 amene sadzapeza zochuluka kwambiri kuposa zimenezi m’nthawi ino, ndipo m’nthawi* ikubwerayo moyo wosatha.”+ Aheberi 10:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pakuti munasonyeza chifundo kwa amene anali m’ndende, ndipo munalola mokondwa kuti katundu wanu alandidwe,+ podziwa kuti inuyo muli ndi chuma chabwino kuposa pamenepo ndiponso chokhalitsa.+
30 amene panopa sadzapeza zochuluka kuwirikiza maulendo 100+ m’nthawi* ino. Iye adzapeza nyumba, abale, alongo, amayi, ana ndi minda, limodzi ndi mazunzo,+ ndipo m’nthawi imene ikubwerayo, adzapeza moyo wosatha.
29 Yesu anawauza kuti: “Ndithu ndikukuuzani, Palibe amene wasiya nyumba, mkazi, abale, makolo kapena ana, chifukwa cha ufumu wa Mulungu+
30 amene sadzapeza zochuluka kwambiri kuposa zimenezi m’nthawi ino, ndipo m’nthawi* ikubwerayo moyo wosatha.”+
34 Pakuti munasonyeza chifundo kwa amene anali m’ndende, ndipo munalola mokondwa kuti katundu wanu alandidwe,+ podziwa kuti inuyo muli ndi chuma chabwino kuposa pamenepo ndiponso chokhalitsa.+