Deuteronomo 33:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munthu amene anauza bambo ndi mayi ake kuti, ‘Sindinawaone.’Ngakhale abale ake sanawavomereze,+Ndipo ana ake sanawadziwe.Pakuti anasunga mawu anu,+Ndipo anapitiriza kusunga pangano lanu.+ Maliko 10:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yesu anati: “Ndithu ndikukuuzani amuna inu, Palibe amene anasiya nyumba, abale, alongo, amayi, abambo, ana kapena minda chifukwa cha ine, ndi chifukwa cha uthenga wabwino,+
9 Munthu amene anauza bambo ndi mayi ake kuti, ‘Sindinawaone.’Ngakhale abale ake sanawavomereze,+Ndipo ana ake sanawadziwe.Pakuti anasunga mawu anu,+Ndipo anapitiriza kusunga pangano lanu.+
29 Yesu anati: “Ndithu ndikukuuzani amuna inu, Palibe amene anasiya nyumba, abale, alongo, amayi, abambo, ana kapena minda chifukwa cha ine, ndi chifukwa cha uthenga wabwino,+