Mateyu 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ndinu odala pamene anthu akukunyozani+ ndi kukuzunzani,+ komanso kukunamizirani zoipa zilizonse chifukwa cha ine. Yohane 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho inunso muli ndi chisoni panopa. Koma ndidzakuonaninso, ndipo mitima yanu idzasangalala.+ Palibenso amene adzathetse chimwemwe chanu. Machitidwe 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 M’malo onsewa anali kulimbitsa mitima ya ophunzira+ ndi kuwalimbikitsa kuti akhalebe m’chikhulupiriro. Anali kuwauza kuti: “Tiyenera kukumana ndi masautso ambiri kuti tikalowe mu ufumu wa Mulungu.”+
11 “Ndinu odala pamene anthu akukunyozani+ ndi kukuzunzani,+ komanso kukunamizirani zoipa zilizonse chifukwa cha ine.
22 Choncho inunso muli ndi chisoni panopa. Koma ndidzakuonaninso, ndipo mitima yanu idzasangalala.+ Palibenso amene adzathetse chimwemwe chanu.
22 M’malo onsewa anali kulimbitsa mitima ya ophunzira+ ndi kuwalimbikitsa kuti akhalebe m’chikhulupiriro. Anali kuwauza kuti: “Tiyenera kukumana ndi masautso ambiri kuti tikalowe mu ufumu wa Mulungu.”+